Mlaliki 2:2 - Buku Lopatulika Ndinati, Kuseka ndi masala; ndi chimwemwe kodi chichita chiyani? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndinati, Kuseka ndi masala; ndi chimwemwe kodi chichita chiyani? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kukakhala kuseka, ndidati, “Imene ija ndi misala.” Chikakhala chisangalatso, ndidati, “Phindu lake nchiyani?” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Kuseka,” ndinati, “imeneyo ndi misala. Ndipo kodi chisangalalo chimabweretsa phindu lanji?” |