Chitsulo chikakhala chosathwa, ndipo ukaleka kunola, uzipambana kulimbikira; koma nzeru ipindulira pochenjeza.
Mlaliki 10:9 - Buku Lopatulika Wosendeza miyala adzaphwetekedwa nayo; wowaza nkhuni nadzitema. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wosendeza miyala adzaphwetekedwa nayo; wowaza nkhuni nadzitema. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Amene amakumba miyala, itha kumpweteka miyalayo. Amene amaŵaza nkhuni, atha kudzipweteka nazo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Amene amaphwanya miyala adzapwetekedwa ndi miyalayo; amene amawaza nkhuni adzapwetekedwa nazo. |
Chitsulo chikakhala chosathwa, ndipo ukaleka kunola, uzipambana kulimbikira; koma nzeru ipindulira pochenjeza.