Mlaliki 10:7 - Buku Lopatulika Ndaona akapolo atakwera pa akavalo, ndi mafumu, alikuyenda pansi ngati akapolo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndaona akapolo atakwera pa akavalo, ndi mafumu, alikuyenda pansi ngati akopolo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndaona akapolo akuyenda pa akavalo, m'menemo akalonga akuyenda pansi ngati akapolo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndaona akapolo atakwera pa akavalo, pamene akalonga akuyenda pansi ngati akapolo. |
amtengere chovala chachifumu amachivala mfumu, ndi kavalo amakwerapo mfumu, naike korona wachifumu pamutu pake,
Wopusa sayenera kukhala ndi zinthu zolongosoka; nanga kapolo ayenera kulamulira akalonga kodi?