Mlaliki 1:12 - Buku Lopatulika Ine Mlaliki ndinali mfumu ya Israele mu Yerusalemu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ine Mlaliki ndinali mfumu ya Israele m'Yerusalemu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ine Mlalikine ndidakhalapo mfumu yolamulira Israele ku Yerusalemu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ine, Mlalikine, ndinali mfumu ya Israeli mu Yerusalemu. |
Taonani, ichi ndachipeza, ati Mlalikiyo, m'kuphatikiza chinthu china ndi chinzake, ndikazindikire malongosoledwe ao;