Mateyu 5:27 - Buku Lopatulika Munamva kuti kunanenedwa, Usachite chigololo; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Munamva kuti kunanenedwa, Usachite chigololo; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Mudamva kuti anthu akale aja adaaŵalamula kuti, ‘Usachite chigololo.’ Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Munamva kuti kunanenedwa kuti, ‘Usachite chigololo.’ |
Munthu akachita chigololo ndi mkazi wa mwini, popeza wachita chigololo ndi mkazi wa mnansi wake, awaphe ndithu, mwamuna ndi mkazi onse awiri.
Munamva kuti kunanenedwa kwa iwo akale, Usaphe; koma yense wakupha adzakhala wopalamula mlandu:
Ndiponso, munamva kuti kunanenedwa kwa iwo akale, Usalumbire konama, koma udzapereka kwa Ambuye zolumbira zako: