Ndipo pamene anasonkhana pamodzi ndi akulu, anakhala upo, napatsa asilikaliwo ndalama zambiri,
Mateyu 28:11 - Buku Lopatulika Ndipo pamene iwo analikupita, onani, ena a alonda anafika kumzinda, nauza ansembe aakulu zonse zimene zinachitidwa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo pamene iwo analikupita, onani, ena a alonda anafika kumzinda, nauza ansembe aakulu zonse zimene zinachitidwa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamene akazi aja ankapita, ena mwa alonda aja adakafika ku mzinda, nakasimbira akulu a ansembe zonse zimene zidaachitika. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Amayi aja akupita, ena mwa alonda aja anapita ku mzinda nafotokozera akulu a ansembe zonse zimene zinachitika. |
Ndipo pamene anasonkhana pamodzi ndi akulu, anakhala upo, napatsa asilikaliwo ndalama zambiri,