mwa iwo amene munali Maria wa Magadala, ndi Maria amake wa Yakobo, ndi wa Yosefe, ndi amake wa ana a Zebedeo.
Mateyu 27:61 - Buku Lopatulika Ndipo Maria wa Magadala anali pamenepo, ndi Maria winayo, anakhala pansi popenyana ndi mandawo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Maria wa Magadala anali pamenepo, ndi Maria winayo, anakhala pansi popenyana ndi mandawo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Maria wa ku Magadala ndi Maria wina uja anali pomwepo atakhala pansi kuyang'anana ndi mandawo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mariya wa Magadala ndi Mariya wina anakhala pansi moyangʼanizana ndi mandawo. |
mwa iwo amene munali Maria wa Magadala, ndi Maria amake wa Yakobo, ndi wa Yosefe, ndi amake wa ana a Zebedeo.
Ndipo popita tsiku la Sabata, mbandakucha, tsiku lakuyamba la sabata, anadza Maria wa Magadala, ndi Maria winayo, kudzaona manda.