Ichi chikhale mphotho ya otsutsana nane yowapatsa Yehova, ndi ya iwo akunenera choipa moyo wanga.
Mateyu 26:66 - Buku Lopatulika muganiza bwanji? Iwo anayankha nati, Ali woyenera kumupha. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 muganiza bwanji? Iwo anayankha nati, Ali woyenera kumupha. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndiye inu mukuganiza bwanji?” Iwo aja adayankha kuti, “Ayenera kuphedwa.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mukuganiza bwanji?” Iwo anayankha kuti, “Ayenera kuphedwa!” |
Ichi chikhale mphotho ya otsutsana nane yowapatsa Yehova, ndi ya iwo akunenera choipa moyo wanga.
Ndipo ansembe ndi aneneri ananena kwa akulu ndi kwa anthu onse, kuti, Munthu uyu ayenera kufa; pakuti wanenera mzinda uwu monga mwamva ndi makutu anu.
Ayuda anamyankha iye, Tili nacho chilamulo ife, ndipo monga mwa chilamulocho ayenera kufa, chifukwa anadziyesera Mwana wa Mulungu.
Ndiye yani wa aneneri makolo anu sanamzunze? Ndipo anawapha iwo amene anaonetseratu za kudza kwake kwa Wolungamayo; wa Iye amene mwakhala tsopano akumpereka ndi akumupha;