Mau a wofuula m'chipululu, Konzani njira ya Yehova, lungamitsani m'dziko loti see khwalala la Mulungu wathu.
Mateyu 24:26 - Buku Lopatulika Onani, Iye ali m'chipululu; musamukeko. Onani, ali m'zipinda; musavomereze. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Onani, ali m'zipinda; musavomereze. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Nchifukwa chake, anthu akadzakuuzani kuti, ‘Inu, Khristu ali ku chipululu,’ musadzapiteko. Kapena akadzati, ‘Ali m'kati mwa nyumba,’ musadzakhulupirire. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Ndiye ngati wina akuwuzani inu kuti, ‘Uyo ali ku chipululu,’ inu musapiteko; kapena akati, ‘Uyu ali kuno mʼchipinda chamʼkati,’ musakhulupirire. |
Mau a wofuula m'chipululu, Konzani njira ya Yehova, lungamitsani m'dziko loti see khwalala la Mulungu wathu.
Pakuti monga mphezi idzera kum'mawa, nionekera kufikira kumadzulo; kotero kudzakhalanso kufika kwake kwa Mwana wa Munthu.
Si ndiwe Mwejipito uja kodi, unachita mipanduko kale lija, ndi kutsogolera ambanda aja zikwi zinai kuchipululu?