Taonani, Ine ndikutumizani inu monga nkhosa pakati pa mimbulu; chifukwa chake khalani ochenjera monga njoka, ndi oona mtima monga nkhunda.
Mateyu 24:25 - Buku Lopatulika Chifukwa chake akanena kwa inu, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Chifukwa chake akanena kwa inu, Onani, Iye ali m'chipululu; musamukeko. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mvetsetsani, Ine ndiye ndakuuziranitu zimenezi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Onani, ndakuwuzani izi nthawi isanafike. |
Taonani, Ine ndikutumizani inu monga nkhosa pakati pa mimbulu; chifukwa chake khalani ochenjera monga njoka, ndi oona mtima monga nkhunda.
chifukwa Akhristu onama adzauka, ndi aneneri onama nadzaonetsa zizindikiro zazikulu ndi zozizwa: kotero kuti akanyenge, ngati nkotheka, osankhidwa omwe. Onani ndakuuziranitu pasadafike.
Ndinanena kale, ndipo ndinena ndisanafikeko, monga pamene ndinali pomwepo kachiwiri kaja, pokhala ine palibe, kwa iwo adachimwa kale ndi kwa onse otsala, kuti, ngati ndidzanso sindidzawaleka;