Nanena naye mfumu, Ufunanji? Nati iye, Mnzanga uyu ananena ndi ine, Tenga mwana wako timudye lero, ndi mwana wanga timudye mawa.
Mateyu 24:18 - Buku Lopatulika ndi iye wa m'munda asabwere kutenga chofunda chake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi iye wa m'munda asabwere kutenga chofunda chake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yemwe ali ku munda, asabwererenso ku nyumba kuti akatenge mwinjiro. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yemwe ali ku munda asapite kukatenga mkanjo wake. |
Nanena naye mfumu, Ufunanji? Nati iye, Mnzanga uyu ananena ndi ine, Tenga mwana wako timudye lero, ndi mwana wanga timudye mawa.
Tsikulo iye amene adzakhala pamwamba pa tsindwi, ndi akatundu ake m'nyumba, asatsike kuwatenga; ndipo iye amene ali m'munda modzimodzi asabwere ku zake za m'mbuyo.