Mateyu 22:34 - Buku Lopatulika Koma Afarisi, pakumva kuti Iye anatontholetsa Asaduki, anasonkhana. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma Afarisi, pakumva kuti Iye anatontholetsa Asaduki, anasonkhana. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Afarisi atamva kuti Yesu adatsutsa Asaduki, adasonkhana. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pakumva kuti Yesu anawakhalitsa chete Asaduki, Afarisi anasonkhana pamodzi. |
Ndipo iye pakuona ambiri a Afarisi ndi a Asaduki akudza ku ubatizo wake, anati kwa iwo, Obadwa a njoka inu, ndani anakulangizani kuthawa mkwiyo ulinkudza?
Ndipo taonani, wachilamulo wina anaimirira namuyesa Iye, nanena, Mphunzitsi, ndidzalowa moyo wosatha ndi kuchita chiyani?