Mateyu 22:26 - Buku Lopatulika chimodzimodzi wachiwiri, ndi wachitatu, kufikira wachisanu ndi chiwiri. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 chimodzimodzi wachiwiri, ndi wachitatu, kufikira wachisanu ndi chiwiri. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Chimodzimodzinso wachiŵiri ndi wachitatu, mpaka wachisanu ndi chiŵiri. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Izi zinachitikiranso mʼbale wa chiwiri ndi wachitatu mpaka wachisanu ndi chiwiri. |
Ndipo anatumiza kwa Iye ophunzira ao, pamodzi ndi Aherode, amene ananena, Mphunzitsi, tidziwa kuti muli woona, ndipo muphunzitsa njira ya Mulungu moona ndithu, ndipo simusamala munthu aliyense; pakuti simuyang'anira pa nkhope ya anthu.
Tsono panali ndi ife abale asanu ndi awiri; ndipo wakuyamba anakwatira, namwalira wopanda mbeu, nasiyira mphwake mkazi wake;