Ndipo tsopano, inu okhala mu Yerusalemu, ndi anthu a Yuda, weruzanitu mlandu wa ine ndi munda wanga wampesa.
Mateyu 21:40 - Buku Lopatulika Tsono atabwera mwini munda, adzachitira olimawo chiyani? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Tsono atabwera mwini munda, adzachitira olimawo chiyani? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Kodi mwini munda wamphesa uja akadzafika, adzaŵatani alimi aja?” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Tsono akabwera mwini munda wamphesa adzachita nawo chiyani matenantiwo?” |
Ndipo tsopano, inu okhala mu Yerusalemu, ndi anthu a Yuda, weruzanitu mlandu wa ine ndi munda wanga wampesa.
Ndipo pamene nyengo ya zipatso inayandikira, anatumiza akapolo ake kwa olima mundawo, kukalandira zipatso zake.
Iwo ananena kwa Iye, Adzaononga koipa oipawo, nadzapereka mundawo kwa olima ena, amene adzambwezera iye zipatso pa nyengo zake.
Pamenepo mwini munda adzachita chiyani? Adzafika, nadzaononga olimawo, nadzapereka mundawo kwa ena.
ndipo mutani, kulanga koposa kotani nanga adzayesedwa woyenera iye amene anapondereza Mwana wa Mulungu, nayesa mwazi wa chipangano umene anayeretsedwa nao chinthu wamba, nachitira chipongwe Mzimu wa chisomo;