Mateyu 19:30 - Buku Lopatulika Koma ambiri oyamba adzakhala akuthungo, ndi akuthungo adzakhala oyamba. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma ambiri oyamba adzakhala akuthungo, ndi akuthungo adzakhala oyamba. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Komatu ambiri amene ali oyambirira adzakhala otsirizira, ndipo amene ali otsirizira adzakhala oyambirira.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma ambiri amene ali oyambirira adzakhala omalizira, ndipo ambiri amene ndi omalizira adzakhala oyambirira.” |
Ndipo onani, alipo akuthungo amene adzakhala oyamba, ndipo alipo oyamba adzakhala akuthungo.
Chifukwa chake tiope kuti kapena likatsala lonjezano lakulowa mpumulo wake, wina wa inu angaoneke ngati adaliperewera.