Mateyu 17:13 - Buku Lopatulika Pomwepo ophunzira anazindikira kuti analankhula nao za Yohane Mbatizi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pomwepo ophunzira anazindikira kuti analankhula nao za Yohane Mbatizi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamenepo ophunzira aja adazindikira kuti ankaŵauza za Yohane Mbatizi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamenepo ophunzira anazindikira kuti amawawuza za Yohane Mʼbatizi. |
koma ndinena kwa inu, kuti Eliya anadza kale, ndipo iwo sanamdziwe iye, koma anamchitira zonse zimene anazifuna iwo. Ndipo chonchonso Mwana wa Munthu adzazunzidwa ndi iwo.
Ndipo pamene iwo anadza kukhamu la anthu, kunafika kwa Iye munthu, namgwadira Iye, nati,