Ndipo anadya onse, nakhuta; ndipo anatola makombo otsala, nadzala madengu khumi ndi iwiri.
Mateyu 16:10 - Buku Lopatulika Penanso mikate isanu ndi iwiri ija ya anthu zikwi zinai, ndi madengu angati munawatola? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Penanso mikate isanu ndi iwiri ija ya anthu zikwi zinai, ndi madengu angati munawatola? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Sujanso ndi buledi msanu ndi muŵiri ndidadyetsa anthu zikwi zinai? Nanga mudaadzaza madengu angati a zotsala? Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kapena buledi musanu ndi muwiri amene anadya anthu 4,000, nanga ndi madengu angati amene munadzaza? |
Ndipo anadya onse, nakhuta; ndipo anatola makombo otsala, nadzala madengu khumi ndi iwiri.