Mateyu 15:16 - Buku Lopatulika Ndipo Iye anati, Kodi inunso mukhala chipulukirire? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Iye anati, Kodi inunso mukhala chipulukirire? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yesu adati, “Kani ngakhale inunso simumvetsa? Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yesu anawafunsa kuti, “Kani ngakhale inunso simumvetsa? |
Bwanji nanga simudziwa kuti sindinanena kwa inu za mikate? Koma pewani chotupitsa cha Afarisi ndi Asaduki.
Kodi chikhalire simudziwa, ndipo simukumbukira mikate isanu ija ya anthu aja zikwi zisanu, ndi madengu angati munawatola?
Ndipo ananena nao, Mutero inunso opanda nzeru kodi? Kodi simuzindikira kuti kanthu kalikonse kochokera kunja kukalowa mwa munthu, sikangathe kumdetsa iye;
Ndipo sanadziwitse kanthu ka izi; ndi mau awa adawabisikira, ndipo sanazindikire zonenedwazo.
Koma iwo sanadziwitse mau awa, ndipo anabisidwa kwa iwo, kuti asawadziwe; ndipo anaopa kumfunsa za mau awa.
Pakuti mungakhale mwayenera kukhala aphunzitsi chifukwa cha nyengoyi, muli nako kusowanso kuti wina aphunzitse inu zoyamba za chiyambidwe cha maneno a Mulungu; ndipo mukhala onga ofuna mkaka, osati chakudya chotafuna.