Ndipo m'mene amuna a pamenepo anamzindikira, anatumiza konse kudziko lonse lozungulira, nadza nao kwa Iye onse akukhala ndi nthenda;
Mateyu 14:34 - Buku Lopatulika Ndipo pamene iwo anaoloka, anafika kumtunda, ku Genesarete. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo pamene iwo anaoloka, anafika kumtunda, ku Genesarete. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono onse adaoloka nyanja nakafika ku Genesarete. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atawoloka, anafika ku Genesareti. |
Ndipo m'mene amuna a pamenepo anamzindikira, anatumiza konse kudziko lonse lozungulira, nadza nao kwa Iye onse akukhala ndi nthenda;
Ndipo panali, pakumkanikiza khamu la anthu, kudzamva mau a Mulungu, Iye analikuimirira m'mbali mwa nyanja ya Genesarete;