Pomwepo Iye anasiya makamuwo, nalowa m'nyumba; ndimo ophunzira ake anadza kwa Iye, nanena, Mutitanthauzire fanizo lija la namsongole wa m'munda.
Mateyu 13:18 - Buku Lopatulika Ndipo tsono mverani inu fanizolo la wofesa mbeu uja. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo tsono mverani inu fanizolo la wofesa mbeu uja. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Tsono inu mumvetse bwino tanthauzo lake la fanizo la munthu wofesa mbeu lija. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Tamverani tsono zimene fanizo la wofesa litanthauza: |
Pomwepo Iye anasiya makamuwo, nalowa m'nyumba; ndimo ophunzira ake anadza kwa Iye, nanena, Mutitanthauzire fanizo lija la namsongole wa m'munda.
Ndipo pamene anakhala pa yekha, iwo amene anali pafupi ndi Iye pamodzi ndi khumi ndi awiriwo anamfunsa za mafanizo.