Ndipo Iye anachokera pamenepo, nalowa m'sunagoge mwao;
Yesu adachoka kumeneko nakaloŵa m'Nyumba yamapemphero.
Atachoka kumeneko anakalowa mʼsunagoge mwawo.