Mukalowa m'tirigu wosasenga wa mnansi wanu, mubudule ngala ndi dzanja lanu, koma musasengako ndi chisenga tirigu wachilili wa mnansi wanu.
Mateyu 12:1 - Buku Lopatulika Nyengo imeneyo Yesu anapita tsiku la Sabata pakati pa minda ya tirigu; ndipo ophunzira ake anali ndi njala, nayamba kubudula ngala, nadya. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Nyengo imeneyo Yesu anapita tsiku la Sabata pakati pa minda ya tirigu; ndipo ophunzira ake anali ndi njala, nayamba kubudula ngala, nadya. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pa tsiku lina la Sabata Yesu ankadutsa m'minda ya tirigu. Ophunzira ake anali ndi njala, ndipo adayamba kuthyolako ngala za tirigu nkumadya. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pa nthawi imeneyo Yesu anadutsa pakati pa minda ya tirigu pa tsiku la Sabata. Ophunzira ake anamva njala nayamba kuthyola ngala za tirigu nʼkumadya. |
Mukalowa m'tirigu wosasenga wa mnansi wanu, mubudule ngala ndi dzanja lanu, koma musasengako ndi chisenga tirigu wachilili wa mnansi wanu.