Mateyu 1:15 - Buku Lopatulika ndi Eliudi anabala Eleazara; ndi Eleazara anabala Matani; ndi Matani anabala Yakobo; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi Eliudi anabala Eleazara; ndi Eleazara anabala Matani; ndi Matani anabala Yakobo; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Eliudi adabereka Eleazara, Eleazara adabereka Matani, Matani adabereka Yakobe. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Eliudi anabereka Eliezara, Eliezara anabereka Matani, Matani anabereka Yakobo. |
ndi Yakobo anabala Yosefe, mwamuna wake wa Maria, amene Yesu, wotchedwa Khristu, anabadwa mwa iye.