Ambuye, mutcherere khutu pemphero la kapolo wanu, ndi pemphero la akapolo anu okondwera nako kuopa dzina lanu; ndipo mupambanitse kapolo wanu lero lino, ndi kumuonetsera chifundo pamaso pa munthu uyu. Koma ndinali ine wothirira mfumu chakumwa chake.
Masalimo 86:6 - Buku Lopatulika Tcherani khutu pemphero langa, Yehova; nimumvere mau a kupemba kwanga. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Tcherani khutu pemphero langa, Yehova; nimumvere mau a kupemba kwanga. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tcherani khutu, Inu Chauta, kuti mumve pemphero langa. Mverani kulira kwanga kopemba. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yehova imvani pemphero langa; mvetserani kulira kwanga kofuna chifundo. |
Ambuye, mutcherere khutu pemphero la kapolo wanu, ndi pemphero la akapolo anu okondwera nako kuopa dzina lanu; ndipo mupambanitse kapolo wanu lero lino, ndi kumuonetsera chifundo pamaso pa munthu uyu. Koma ndinali ine wothirira mfumu chakumwa chake.
Yehova, imvani chilungamo, mverani mfuu wanga; tcherani khutu ku pemphero langa losatuluka m'milomo ya chinyengo.