Masalimo 83:17 - Buku Lopatulika Achite manyazi, naopsedwe kosatha; ndipo asokonezeke, naonongeke. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Achite manyazi, naopsedwe kosatha; ndipo asokonezeke, naonongeke. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Achitedi manyazi ndi mantha mpaka muyaya, ndipo afe imfa yonyozeka. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Achite manyazi ndi mantha nthawi zonse; awonongeke mwa manyazi. |
Achite manyazi, nadodome iwo akukondwera chifukwa cha choipa chidandigwera. Avekeke ndi manyazi ndi kupunzika iwo akudzikuza pa ine.
Athe nzeru nachite manyazi iwo akufuna moyo wanga; abwezedwe m'mbuyo nasokonezeke iwo akundipangira chiwembu.