Ndikakhala woipa, tsoka ine; ndikakhala wolungama, sindidzakweza mutu wanga; ndadzazidwa ndi manyazi, koma penyani kuzunzika kwanga.
Masalimo 83:16 - Buku Lopatulika Achititseni manyazi pankhope pao; kuti afune dzina lanu, Yehova. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Achititseni manyazi pankhope pao; kuti afune dzina lanu, Yehova. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Inu Chauta, muŵachititse manyazi, kuti azifunafuna dzina lanu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Muphimbe nkhope zawo ndi manyazi kuti adzafunefune dzina lanu Yehova. |
Ndikakhala woipa, tsoka ine; ndikakhala wolungama, sindidzakweza mutu wanga; ndadzazidwa ndi manyazi, koma penyani kuzunzika kwanga.
Adzachita manyazi, nadzanthunthumira kwakukulu adani anga onse; adzabwerera, nadzachita manyazi modzidzimuka.