Pamene mulanga munthu ndi zomdzudzula chifukwa cha mphulupulu, mukanganula kukongola kwake monga mumachita ndi njenjete. Indedi, munthu aliyense ali chabe.
Masalimo 80:16 - Buku Lopatulika Unapserera ndi moto, unadulidwa; aonongeka pa kudzudzula kwa nkhope yanu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Unapserera ndi moto, unadulidwa; aonongeka pa kudzudzula kwa nkhope yanu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adani athu autentha, augwetsa pansi. Ayang'aneni iwowo mokwiya ndi kuŵaononga. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mpesa wanu wadulidwa ndi kutenthedwa ndi moto; pakudzudzula kwanu anthu anu awonongeka. |
Pamene mulanga munthu ndi zomdzudzula chifukwa cha mphulupulu, mukanganula kukongola kwake monga mumachita ndi njenjete. Indedi, munthu aliyense ali chabe.
Ponyala nthambi zake zidzathyoledwa; akazi adzafika, nazitentha ndi moto, pakuti ali anthu opanda nzeru; chifukwa chake Iye amene anawalenga sadzawachitira chisoni, ndi Iye amene anawaumba sadzawakomera mtima.
Ngati wina sakhala mwa Ine, watayika kunja monga nthambi, nafota; ndipo azisonkhanitsa nazitaya kumoto, nazitentha.
amene adzamva chilango, ndicho chionongeko chosatha chowasiyanitsa kunkhope ya Ambuye, ndi kuulemerero wa mphamvu yake,