Ndipo Hiramu mfumu ya ku Tiro anatuma anyamata ake kwa Solomoni, popeza anamva kuti adamdzoza mfumu m'malo mwa atate wake; pakuti Hiramu adakondana ndi Davide masiku onse.
Masalimo 80:12 - Buku Lopatulika Munapasuliranji maphambo ake, kotero kuti onse akupita m'njira atcherako? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Munapasuliranji maphambo ake, kotero kuti onse akupita m'njira atcherako? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Nanga chifukwa chiyani mwagumula mpanda wake, kuti opita m'njira azithyola nawo zipatso zake? Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Chifukwa chiyani mwagwetsa makoma ake kuti onse amene akudutsa athyole mphesa zake? |
Ndipo Hiramu mfumu ya ku Tiro anatuma anyamata ake kwa Solomoni, popeza anamva kuti adamdzoza mfumu m'malo mwa atate wake; pakuti Hiramu adakondana ndi Davide masiku onse.
Ndipo tsopano ndidzakuuzani chimene nditi ndichite ndi munda wanga wampesa; ndidzachotsapo tchinga lake, ndipo zidzadyedwa; ndidzagumula linga lake ndipo zidzapondedwa pansi;
Pakuti Yehova abwezeranso ukulu wake wa Yakobo ngati ukulu wake wa Israele; pakuti okhuthula anawakhuthula, naipsa nthambi zake za mpesa.
Iye adzafika nadzaononga olima munda aja, nadzapatsa munda kwa ena. Ndipo pamene iwo anamva, anati, Musatero iai!