Mthunzi wake unaphimba mapiri, ndi nthambi zake zikunga mikungudza ya Mulungu.
Mapiri adaphimbidwa ndi mthunzi wake, mikungudza yaikulu yomwe idaphimbidwa ndi nthambi zake.
Mapiri anaphimbidwa ndi mthunzi wake, mikungudza yamphamvu ndi nthambi zake.
Mitengo ya Yehova yadzala ndi madzi; mikungudza ya ku Lebanoni imene anaioka;
Ndipo ndinatuma mavu atsogolere inu, amene anawaingitsa pamaso panu, ndiwo mafumu awiri a Aamori; osati ndi lupanga lako, kapena ndi uta wako ai.