Masalimo 76:4 - Buku Lopatulika Inu ndinu wakuunikira, ndi womveka wakuposa mapiri muli achifwamba. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Inu ndinu wakuunikira, ndi womveka wakuposa mapiri muli achifwamba. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Inu Mulungu, mukuwonetsa ulemerero ndi mphamvu kupambana mapiri a zofunkha. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Wolemekezeka ndinu, wamphamvu kuposa mapiri amene ali ndi nyama zambiri. |
Mkango wakwera kutuluka m'nkhalango mwake, ndipo waononga amitundu ali panjira, watuluka m'mbuto mwake kuti achititse dziko lako bwinja, kuti mizinda yako ipasuke mulibenso wokhalamo.
Ndipo unayendayenda pakati pa mikango, nukhala msona, nuphunzira kugwira nyama, nulusira anthu.
ndipo ndidzakantha uta wako kuuchotsa m'dzanja lako lamanzere, ndi kutayitsa mivi yako kudzanja lako lamanja.