Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




Masalimo 74:5 - Buku Lopatulika

Anaoneka ngati osamula nkhwangwa kunkhalango.

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Anaoneka ngati osamula nkhwangwa kunkhalango.

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Adadulamo zonse, monga momwe anthu amadulira mitengo m'nkhalango.

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Iwo anachita ngati anthu oti anyamula mbendera zawo kuti adule mitengo mʼnkhalango.

Onani mutuwo



Masalimo 74:5
3 Mawu Ofanana  

Ndipo tsono, lamulirani kuti anditemere mitengo yamkungudza ku Lebanoni, ndipo akapolo anga adzakhala ndi akapolo anu, ndipo ndidzakupatsani mphotho ya akapolo anu monga mudzanena; popeza mudziwa kuti pakati pa ife palibe mmisiri wakudziwa kutema mitengo ngati anthu a ku Sidoni.


ndiye mwana wa munthu wamkazi wa ana aakazi a Dani, ndipo atate wake ndiye munthu wa ku Tiro, wodziwa kuchita ndi golide, ndi siliva, ndi mkuwa, ndi chitsulo, ndi mwala, ndi mitengo, ndi thonje lofiirira, ndi lamadzi, ndi bafuta la thonje losansitsa ndi lofiira, ndi kuzokota mazokotedwe ali onse, ndi kulingirira chopanga chilichonse; kuti ampatse pokhala pamodzi ndi aluso anu, ndi aluso a mbuye wanga Davide atate wanu.