Masalimo 73:5 - Buku Lopatulika Savutika monga anthu ena; sasautsika monga anthu ena. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Savutika monga anthu ena; sasautsika monga anthu ena. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Saona mavuto monga anthu ena, sazunzika ngati anzao. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Saona mavuto monga anthu ena; sazunzika ngati anthu ena onse. |
Koma poweruzidwa, tilangidwa ndi Ambuye, kuti tingatsutsidwe pamodzi ndi dziko lapansi.
Koma ngati mukhala opanda chilango, chimene onse adalawako, pamenepo muli am'thengo, si ana ai.
Onse amene ndiwakonda, ndiwadzudzula ndi kuwalanga; potero chita changu, nutembenuke mtima.