Pakuti m'dzanja la Yehova muli chikho; ndi vinyo wake achita thovu; chidzala ndi zosakanizira, ndipo atsanulako. Indedi, oipa onse a padziko lapansi adzamwa nadzagugudiza nsenga zake.
Masalimo 73:10 - Buku Lopatulika Chifukwa chake anthu ake amabwera kudza kuno, ndipo chikho chodzala ndi madzi achigugudiza. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Chifukwa chake anthu ake amabwera kudza kuno, ndipo chikho chodzala ndi madzi achigugudiza. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Nchifukwa chake ngakhale anthu a Mulungu amabwera kwa iwo, ndipo amakhuta zonena zao ngati madzi akumwa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Nʼchifukwa chake anthu awo amapita kwa iwowo ndi kumwa madzi mochuluka. |
Pakuti m'dzanja la Yehova muli chikho; ndi vinyo wake achita thovu; chidzala ndi zosakanizira, ndipo atsanulako. Indedi, oipa onse a padziko lapansi adzamwa nadzagugudiza nsenga zake.