Ndipo mau otsiriza a Davide ndi awa: Atero Davide mwana wa Yese, atero munthu wokwezedwa, ndiye wodzozedwa wa Mulungu wa Yakobo, ndi mwini nyimbo yokoma ya Israele.
Masalimo 72:20 - Buku Lopatulika Mapemphero a Davide mwana wa Yese atha. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mapemphero a Davide mwana wa Yese atha. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ano ndiwo mathero a mapemphero a Davide, mwana wa Yese. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Uku ndiko kumaliza kwa mapemphero a Davide mwana wa Yese. |
Ndipo mau otsiriza a Davide ndi awa: Atero Davide mwana wa Yese, atero munthu wokwezedwa, ndiye wodzozedwa wa Mulungu wa Yakobo, ndi mwini nyimbo yokoma ya Israele.
nuti, Chomwecho adzamira Babiloni, sadzaukanso chifukwa cha choipa chimene ndidzamtengera iye; ndipo adzatopa. Mau a Yeremiya ndi omwewo.