Mwayesera mtima wanga; mwandizonda usiku; mwandisuntha, simupeza kanthu; mwatsimikiza mtima kuti m'kamwa mwanga simudzalakwa.
Masalimo 69:5 - Buku Lopatulika Mulungu, mudziwa kupusa kwanga; ndipo kutsutsika kwanga sikubisikira Inu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mulungu, mudziwa kupusa kwanga; ndipo kutsutsika kwanga sikubisikira Inu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Inu Mulungu, mumadziŵa kupusa kwanga, zolakwa zanga sizili zobisika pamaso panu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mukudziwa uchitsiru wanga, Inu Mulungu, kulakwa kwanga sikuli kobisika kwa Inu. |
Mwayesera mtima wanga; mwandizonda usiku; mwandisuntha, simupeza kanthu; mwatsimikiza mtima kuti m'kamwa mwanga simudzalakwa.
Adani anga asandikondwerere ine monyenga; okwiya nane kopanda chifukwa asanditsinzinire.
Ambuye, chikhumbo changa chonse chili pamaso panu; ndipo kubuula kwanga sikubisika kwa Inu.
Pakuti maso anga ali panjira zao zonse, sabisika pa nkhope yanga, mphulupulu yao siibisika pamaso panga.