Masalimo 66:18 - Buku Lopatulika Ndikadasekera zopanda pake m'mtima mwanga, Ambuye sakadamvera. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndikadasekera zopanda pake m'mtima mwanga, Ambuye sakadamvera. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndikadazindikira choipa chilichonse mumtima mwanga ndi kuchibisa, Ambuye sakadandimvera. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndikanasekerera tchimo mu mtima mwanga Ambuye sakanamvera; |
Ndipo pamene mutambasula manja anu, ndidzakubisirani inu maso anga; inde pochulukitsa mapemphero anu Ine sindidzamva; manja anu adzala mwazi.
Tidziwa kuti Mulungu samvera ochimwa. Koma ngati munthu aliyense akhala wopembedza Mulungu nachita chifuniro chake, amvera ameneyo.
Mupempha, ndipo simulandira, popeza mupempha koipa, kuti mukachimwaze pochita zikhumbitso zanu.