Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




Masalimo 61:6 - Buku Lopatulika

Mudzatalikitsa moyo wa mfumu. Zaka zake zidzafikira mibadwomibadwo.

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Mudzatalikitsa moyo wa mfumu. Zaka zake zidzafikira mibadwomibadwo.

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Talikitsani moyo wa mfumu, zaka zake zifikire ku mibadwo ndi mibadwo.

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Wonjezerani masiku a moyo wa mfumu, zaka zake kwa mibado yochuluka.

Onani mutuwo



Masalimo 61:6
7 Mawu Ofanana  

Yehova ndiye gawo la cholowa changa ndi chikho changa, ndinu wondigwirira cholandira changa.


Zingwe zandigwera mondikondweretsa; inde cholowa chokoma ndili nacho.


Anakupemphani moyo, mwampatsa iye; mwamtalikitsira masiku kunthawi za nthawi.


Pakuti mumuikira madalitso kunthawi zonse; mumkondweretsa ndi chimwemwe pankhope panu.


Koma kunakomera Yehova kumtundudza; anammvetsa zowawa; moyo wake ukapereka nsembe yopalamula, Iye adzaona mbeu yake, adzatanimphitsa masiku ake; ndipo chomkondweretsa Yehova chidzakula m'manja mwake.