Masalimo 59:8 - Buku Lopatulika Koma Inu, Yehova, mudzawaseka; mudzalalatira amitundu onse. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma Inu, Yehova, mudzawaseka; mudzalalatira amitundu onse. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma Inu Chauta, mumangoŵaseka. Inu mumanyozera anthu onse akunja. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma Inu Yehova, mumawaseka, mumayinyoza mitundu yonseyo. |
Mukwezeke m'mwambamwamba, Mulungu; ulemerero wanu ukhale pamwamba padziko lonse lapansi.
Ndinu Yehova, Mulungu wa makamu, Mulungu wa Israele. Ukani kukazonda amitundu onse, musachitire chifundo mmodzi yense wakuchita zopanda pake monyenga.
Ndipo ngati iye samvera iwo, uuze Mpingo; ndipo ngati iye samveranso Mpingowo, akhale kwa iwe monga wakunja ndi wamsonkho.