Muwakumbukire Mulungu wanga, popeza anadetsa unsembe, ndi pangano la unsembe, ndi la Alevi.
Masalimo 59:6 - Buku Lopatulika Abwera madzulo, auwa ngati galu, nazungulira mzinda. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Abwera madzulo, auwa ngati galu, nazungulira mudzi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Amabweranso madzulo aliwonse akuuwa ngati agalu, nkumangoyendayenda mu mzinda. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iwo amabweranso madzulo akuchita phokoso ngati agalu ndi kumangoyendayenda mu mzinda. |
Muwakumbukire Mulungu wanga, popeza anadetsa unsembe, ndi pangano la unsembe, ndi la Alevi.
Pakuti andizinga agalu, msonkhano wa oipa wanditsekereza; andiboola m'manja anga ndi m'mapazi anga.
Ndipo Saulo anatumiza mithenga kunyumba ya Davide imdikire, ndi kumupha m'mawa; koma Mikala mkazi wa Davide anamuuza, nati, Ukapanda kupulumutsa moyo wako usiku uno, udzaphedwa ndithu m'mawa.