Penyani, ndiyankheni, Yehova Mulungu wanga. Penyetsani maso anga, kuti ndingagone tulo ta imfa;
Masalimo 54:2 - Buku Lopatulika Imvani pemphero langa, Mulungu; tcherani khutu mau a pakamwa panga. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Imvani pemphero langa, Mulungu; tcherani khutu mau a pakamwa panga. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Inu Mulungu, imvani pemphero langa, tcherani khutu kuti mumve mau a pakamwa panga. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Imvani pemphero langa, Inu Mulungu mvetserani mawu a pakamwa panga. |
Penyani, ndiyankheni, Yehova Mulungu wanga. Penyetsani maso anga, kuti ndingagone tulo ta imfa;
Fulumirani ndiyankheni, Yehova; mzimu wanga ukutha. Musandibisire nkhope yanu; ndingafanane nao akutsikira kudzenje.
Ndipo a ku Zifi anakwera kwa Saulo ku Gibea, nati, Davide salikubisala kwathu kodi, m'ngaka za m'nkhalango ku Horesi, m'phiri la Hakila, limene lili kumwera kwa chipululu?
Ndipo Azifi anafika kwa Saulo ku Gibea, nati, Kodi Davide sali kubisala m'phiri la Hakila, kupenya kuchipululu!