Masalimo 50:8 - Buku Lopatulika Sindikudzudzula iwe chifukwa cha nsembe zako; popeza nsembe zako zopsereza zili pamaso panga chikhalire. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Sindikudzudzula iwe chifukwa cha nsembe zako; popeza nsembe zako zopsereza zili pamaso panga chikhalire. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Sindikudzudzulani chifukwa cha nsembe zanu, popeza kuti mumapereka nsembe zanu zopsereza kwa Ine nthaŵi zonse. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Sindikudzudzula chifukwa cha nsembe zako, kapena nsembe zako zopsereza zimene zili pamaso panga nthawi zonse. |
Pakuti ndikondwera nacho chifundo, si nsembe ai; ndi kumdziwa Mulungu kuposa nsembe zopsereza.