Masalimo 49:8 - Buku Lopatulika Popeza chiombolo cha moyo wao ncha mtengo wake wapatali, ndipo chilekeke nthawi zonse. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Popeza chiombolo cha moyo wao ncha mtengo wake wapatali, ndipo chilekeke nthawi zonse. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Popeza kuti choombolera moyo wa munthu ndi chamtengowapatali, ndipo sangathe kuchikwanitsa, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Dipo la moyo ndi la mtengowapatali, palibe malipiro amene angakwanire, |
Chilikuti chifundo chanu chakale, Ambuye, munachilumbirira Davide pa chikhulupiriko chanu?
Pakuti munthu adzapindulanji, akalandira dziko lonse, nataya moyo wake? Kapena munthu adzaperekanji chosintha ndi moyo wake?