Masalimo 41:11 - Buku Lopatulika Umo ndidziwa kuti mukondwera ndi ine, popeza mdani wanga sandiseka. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Umo ndidziwa kuti mukondwera ndi ine, popeza mdani wanga sandiseka. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mukatero ndidzadziŵa kuti mumakondwera nane, chifukwa mdani wanga sadandipambane. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ine ndikudziwa kuti mukukondwera nane, pakuti mdani wanga sandigonjetsa. |
kuti anganene mdani wanga, Ndamgonjetsa; ndipo angakondwere otsutsana nane posunthika ine.
Mundichitire chizindikiro choti chabwino; kuti ondida achione, nachite manyazi, popeza Inu, Yehova, munandithandiza ndi kundisangalatsa.
Muimbire Yehova, mulemekeze Yehova; pakuti walanditsa moyo wa aumphawi m'dzanja la ochita zoipa.