Ndipo ndinati kwa mfumu, Mfumu ikhale ndi moyo kosatha; ilekerenji nkhope yanga kuchita chisoni, popeza pali bwinja kumzinda kuli manda a makolo anga, ndi zipata zake zopsereza ndi moto.
Masalimo 38:7 - Buku Lopatulika Pakuti m'chuuno mwanga mutentha kwambiri; palibe pamoyo m'mnofu mwanga. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pakuti m'chuuno mwanga mutentha kwambiri; palibe pamoyo m'mnofu mwanga. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Thupi langa likutentha kwambiri ndi malungo, ndipo lilibe nyonga. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Msana wanga wagwidwa ndi ululu wosasimbika, mulibe thanzi mʼthupi langa. |
Ndipo ndinati kwa mfumu, Mfumu ikhale ndi moyo kosatha; ilekerenji nkhope yanga kuchita chisoni, popeza pali bwinja kumzinda kuli manda a makolo anga, ndi zipata zake zopsereza ndi moto.
Mwa mphamvu yaikulu ya nthenda yanga chovala changa chinasandulika, chindithina ngati pakhosi pa malaya anga.
Ndipo pomwepo mngelo wa Ambuye anamkantha, chifukwa sanampatse Mulungu ulemerero; ndipo anadyedwa ndi mphutsi, natsirizika.