Masalimo 38:16 - Buku Lopatulika Pakuti ndinati, Asakondwerere ine; pakuterereka phazi langa, asadzikuze pa ine. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pakuti ndinati, Asakondwerere ine; pakuterereka phazi langa, asadzikuze pa ine. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Popeza ndimapemphera kuti, “Musalole konse kuti akondwerere pa ine, amene amandinyodola akaona kuti ndikuterereka.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pakuti Ine ndinati, “Musawalole kuti akondwere kapena kudzikweza okha pa ine pamene phazi langa laterereka.” |
Kubwezera chilango nkwanga, kubwezera komwe, pa nyengo ya kuterereka phazi lao; pakuti tsiku la tsoka lao layandika, ndi zinthu zowakonzeratu zifulumira kudza.