nati, Ndinatuluka m'mimba ya mai wanga wamaliseche, wamaliseche ndidzamukanso; Yehova anapatsa, Yehova watenga, lidalitsike dzina la Yehova.
Masalimo 34:2 - Buku Lopatulika Moyo wanga udzatamanda Yehova; ofatsa adzakumva nadzakondwera. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Moyo wanga udzatamanda Yehova; ofatsa adzakumva nadzakondwera. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Moyo wanga umanyadira Chauta. Anthu ozunzika amve ndipo akondwere. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Moyo wanga udzanyadira Yehova; anthu osautsidwa amve ndi kukondwera. |
nati, Ndinatuluka m'mimba ya mai wanga wamaliseche, wamaliseche ndidzamukanso; Yehova anapatsa, Yehova watenga, lidalitsike dzina la Yehova.
Tulutsani moyo wanga m'ndende, kuti ndiyamike dzina lanu; olungama adzandizinga; pakuti mudzandichitira zokoma.
koma wakudzitamandira adzitamandire adzikweze umo, kuti ali wakuzindikira, ndi kundidziwa Ine, kuti ndine Yehova wakuchita zokoma mtima, chiweruziro, ndi chilungamo m'dziko lapansi, pakuti m'menemo ndikondwerera, ati Yehova.