Ndinafuulira kwa Inu, Yehova; kwa Ambuye ndinapemba,
Ndinafuulira kwa Inu, Yehova; kwa Yehova ndinapemba,
Pamenepo ndidalirira Inu Chauta, ndipo ndidapempha chifundo chanu kuti,
Kwa Inu Yehova ndinayitana; kwa Ambuye ndinapempha chifundo;
Koma tsopano chakufikira iwe, ndipo ukomoka; chikukhudza, ndipo uvutika.
Munthu uyu wozunzika anafuula, ndipo Yehova anamumva, nampulumutsa m'masautso ake onse.