Masalimo 22:19 - Buku Lopatulika Koma Inu, Yehova, musakhale kutali; mphamvu yanga Inu, mufulumire kundithandiza. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma Inu, Yehova, musakhale kutali; mphamvu yanga Inu, mufulumire kundithandiza. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma Inu Chauta musakhale kutali. Inu, mphamvu zanga, fulumirani kudzandithandiza. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma Inu Yehova, musakhale kutali; Inu mphamvu yanga, bwerani msanga kuti mudzandithandize. |
Ndipo ine ndine wozunzika ndi waumphawi; koma Ambuye andikumbukira ine. Inu ndinu mthandizi wanga, ndi Mpulumutsi wanga, musamachedwa, Mulungu wanga.
Koma ine ndine wozunzika ndi waumphawi; mundifulumirire, Mulungu. Inu ndinu mthandizi wanga ndi Mpulumutsi wanga; musachedwe, Yehova.