Agawana zovala zanga, nachita maere pa malaya anga.
Agaŵana zovala zanga, ndipo achitira malaya anga maere.
Iwo agawana zovala zanga pakati pawo ndi kuchita maere pa zovala zangazo.
Ndipo pamene anampachika Iye, anagawana zovala zake ndi kulota maere:
Ndipo anampachika Iye, nagawana zovala zake mwa iwo okha, ndi kuchita maere pa izo, kuti adziwe yense adzatenga chiyani.
Ndipo Yesu ananena, Atate, muwakhululukire iwo, pakuti sadziwa chimene achita. Ndipo anagawana zovala zake, poyesa maere.