Ngati ndachimwa, ndingachitire Inu chiyani, Inu wodikira anthu? Mwandiikiranji ndikhale chandamali chanu? Kuti ndikhale kwa ine ndekha katundu?
Masalimo 21:12 - Buku Lopatulika Pakuti mudzawabweza m'mbuyo, popiringidza m'nsinga zanu pankhope pao. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pakuti mudzawabweza m'mbuyo, popiringidza m'nsinga zanu pankhope pao. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa pakuti idzaŵapirikitsa potendekera nkhope zao ndi mauta ake. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero pakuti mudzawapirikitsa ndipo adzaonetsa misana yawo pamene mudzawaloza ndi mivi yanu. |
Ngati ndachimwa, ndingachitire Inu chiyani, Inu wodikira anthu? Mwandiikiranji ndikhale chandamali chanu? Kuti ndikhale kwa ine ndekha katundu?
Pamenepo adani anga adzabwerera m'mbuyo tsiku lakuitana ine. Ichi ndidziwa, kuti Mulungu avomerezana nane.
Panganani upo, koma udzakhala chabe; nenani mau, koma sadzachitika; pakuti Mulungu ali pamodzi ndi ife.